Levitiko 4:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo achotse mafuta onse a ng'ombe ya nsembe yauchimo, achotse mafuta akukuta matumbo, ndi mafuta onse akukhala pamatumbo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo achotse mafuta onse a ng'ombe ya nsembe yauchimo, achotse mafuta akukuta matumbo, ndi mafuta onse akukhala pamatumbo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono mafuta onse a ng'ombe yamphongo yoperekera nsembe yopepesera machimoyo, aŵachotse pamodzi ndi mafuta okuta matumbo, ndiponso mafuta ena onse okhala pamatumbopo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pambuyo pake achotse mafuta onse a ngʼombe yayimuna yopepesera machimoyo: mafuta okuta zamʼkati kapena mafuta onse amʼkatimo. Onani mutuwo |