Levitiko 4:9 - Buku Lopatulika9 ndi impso ziwiri ndi mafuta ali pomwepo, okhala m'chuuno, ndi chokuta cha mphafa chofikira kuimpso, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 ndi impso ziwiri ndi mafuta ali pomwepo, okhala m'chuuno, ndi chokuta cha mphafa chofikira kuimpso, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Achotsenso imso ziŵiri pamodzi ndi mafuta ake omwe cham'chiwunomu, ndiponso mphumphu za mafuta akuchiŵindi ochotsa pamodzi ndi imso zija, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Achotsenso ndi kubwera ndi impsyo zonse ziwiri pamodzi ndi mafuta onse ndiponso mafuta onse amene aphimba chiwindi ndi impsyo Onani mutuwo |