Levitiko 4:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo wansembeyo atengeko mwazi, nauike pa nyanga za guwa la nsembe la chofukiza cha fungo lokoma, lokhala m'chihema chokomanako pamaso pa Yehova; nathire mwazi wonse wa ng'ombeyo patsinde paguwa la nsembe yopsereza, lokhala pa khomo la chihema chokomanako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo wansembeyo atengeko mwazi, nauike pa nyanga za guwa la nsembe la chofukiza cha fungo lokoma, lokhala m'chihema chokomanako pamaso pa Yehova; nathire mwazi wonse wa ng'ombeyo patsinde pa guwa la nsembe yopsereza, lokhala pa khomo la chihema chokomanako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Pambuyo pake wansembe apakeko magaziwo pa nyanga za guwa la m'chihema chamsonkhano lofukizirapo lubani wonunkhira fungo lokoma pamaso pa Chauta. Magazi ena otsala a ng'ombeyo aŵathire pa tsinde la guwa la nsembe zopsereza, limene lili pa khomo la chihema chamsonkhano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Kenaka wansembe apake magaziwo pa nyanga za guwa lofukizira lubani limene lili pamaso pa Yehova mu tenti ya msonkhano. Magazi ena otsalawo awathire pa tsinde pa guwa lansembe zopsereza, limene lili pa khomo la tenti ya msonkhano. Onani mutuwo |