Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Levitiko 4:16 - Buku Lopatulika

16 Ndipo wansembe wodzozedwayo adze nao mwazi wina wa ng'ombeyo ku chihema chokomanako;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ndipo wansembe wodzozedwayo adze nao mwazi wina wa ng'ombeyo ku chihema chokomanako;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Wansembe wodzozedwa atengeko magazi a ng'ombe yamphongoyo ndi kubwera nawo ku chihema chamsonkhano.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Tsono wansembe wodzozedwa atengeko magazi a ngʼombeyo ndi kulowa nawo mu tenti ya msonkhano.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 4:16
4 Mawu Ofanana  

Ndipo akulu a khamulo aike manja ao pamutu pa ng'ombeyo, pamaso pa Yehova; naiphe ng'ombeyo pamaso pa Yehova.


naviike chala chake m'mwazi wa nsembewo, nauwaze kasanu ndi kawiri pamaso pa Yehova, chakuno cha nsalu yotchinga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa