Levitiko 4:17 - Buku Lopatulika17 naviike chala chake m'mwazi wa nsembewo, nauwaze kasanu ndi kawiri pamaso pa Yehova, chakuno cha nsalu yotchinga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 naviike chala chake m'mwazi wa nsembewo, nauwaze kasanu ndi kawiri pamaso pa Yehova, chakuno cha nsalu yotchinga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Pamenepo wansembeyo aviike chala chake m'magazi, ndipo pamaso pa Chauta awaze magaziwo kasanu ndi kaŵiri patsogolo pa nsalu yochinga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Aviyike chala chake mʼmagaziwo ndi kuwawaza pamaso pa Yehova kasanu ndi kawiri patsogolo pa nsalu yotchinga. Onani mutuwo |