Levitiko 3:8 - Buku Lopatulika8 naike dzanja lake pamutu pa chopereka chake, naiphe patsogolo pa chihema chokomanako; ndipo ana a Aroni awaze mwazi wake paguwa la nsembe pozungulira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 naike dzanja lake pamutu pa chopereka chake, naiphe patsogolo pa chihema chokomanako; ndipo ana a Aroni awaze mwazi wake pa guwa la nsembe pozungulira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Asanjike dzanja lake pamutu pa nkhosayo, ndipo aiphere pa khomo la chihema chamsonkhano. Pambuyo pake ana a Aroni aliwaze magazi guwa molizungulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Asanjike dzanja lake pamutu pa nkhosayo ndipo ayiphere pa khomo la tenti ya msonkhano. Ndipo ana a Aaroni awaze magaziwo mbali zonse za guwalo. Onani mutuwo |