Levitiko 3:7 - Buku Lopatulika7 akabwera nayo nkhosa kuti ikhale chopereka chake, abwere nayo pamaso pa Yehova; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 akabwera nayo nkhosa kuti ikhale chopereka chake, abwere nayo pamaso pa Yehova; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Akapereka nkhosa kuti ikhale nsembe, abwere nayo pamaso pa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ngati apereka nsembe ya mwana wankhosa, abwere naye pamaso pa Yehova. Onani mutuwo |