Levitiko 3:10 - Buku Lopatulika10 ndi impso ziwiri, ndi mafuta ali pomwepo, okhala m'chuuno, ndi chokuta cha mphafa chofikira kuimpso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 ndi impso ziwiri, ndi mafuta ali pomwepo, okhala m'chuuno, ndi chokuta cha mphafa chofikira kuimpso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 impso ziŵiri pamodzi ndi mafuta ake omwe, ndiponso mphumphu ya mafuta akuchiŵindi, ochotsa pamodzi ndi imso zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 impsyo zonse ziwiri pamodzi ndi mafuta amene akuta impsyozo, msonga ya chiwindi imene idzachotsedwere limodzi ndi impsyozo. Onani mutuwo |