Levitiko 26:2 - Buku Lopatulika2 Musunge masabata anga, ndi kuchitira ulemu malo anga opatulika; Ine ndine Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Musunge masabata anga, ndi kuchitira ulemu malo anga opatulika; Ine ndine Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Muzisunga masiku anga a Sabata ndi kulemekeza malo anga oyera. Ine ndine Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “ ‘Muzisunga Masabata anga ndipo muzilemekeza malo anga wopatulika. Ine ndine Yehova. Onani mutuwo |