Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Levitiko 2:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo ubwere nayo nsembe yaufa yopangika ndi izi kwa Yehova; ndipo atabwera nacho kwa wansembe, iyeyo apite nacho ku guwa la nsembe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo ubwere nayo nsembe yaufa yopangika ndi izi kwa Yehova; ndipo atabwera nacho kwa wansembe, iyeyo apite nacho ku guwa la nsembe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Tsono ubwere nacho chopereka chimenechi kwa Chauta, ndipo utachipereka kwa wansembe, iyeyo abwere nacho ku guwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Munthu azibwera ndi nsembe za chakudya zimene wapanga ndi zinthu zimenezi. Atachipereka kwa wansembe, iyeyu adzipita nacho ku guwa.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 2:8
3 Mawu Ofanana  

Mudzimangire chiguduli m'chuuno mwanu, nimulire, ansembe inu; bumani otumikira kuguwa la nsembe inu; lowani, gonani usiku wonse m'chiguduli, inu otumikira Mulungu wanga; pakuti nsembe yaufa ndi nsembe yothira zaletsedwera nyumba ya Mulungu wanu.


Ndipo chopereka chako chikakhala nsembe yaufa ya mumphika, chikhale cha ufa wosalala ndi mafuta.


Ndipo wansembeyo atengeko chikumbutso pa nsembe yaufa, nachitenthe paguwa la nsembe; ndicho nsembe yamoto ya fungo lokoma la kwa Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa