Levitiko 2:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo chopereka chako chikakhala nsembe yaufa ya mumphika, chikhale cha ufa wosalala ndi mafuta. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo chopereka chako chikakhala nsembe yaufa ya mumphika, chikhale cha ufa wosalala ndi mafuta. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ndipo nsembe yako ikakhala ya chopereka cha chakudya chophika pa chiwaya, chikhale ya ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ngati nsembe yako yachakudya ndi yophikidwa pa chiwaya, ikhale ya buledi wa ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta. Onani mutuwo |