Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Levitiko 2:6 - Buku Lopatulika

6 Uphwanye, nuthirepo mafuta; ndiyo nsembe yaufa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Uphwanye, nuthirepo mafuta; ndiyo nsembe yaufa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Umuduledule ndi kumupaka mafuta. Chimenecho ndicho chopereka cha chakudya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Umuduledule bulediyo ndi kumupaka mafuta; imeneyo ndi nsembe yachakudya.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 2:6
6 Mawu Ofanana  

Ndipo asende nsembe yopsereza, ndi kuikadzula ziwalo zake.


Ndipo nsembe yaufa yako ikakhala yokazinga m'chiwaya, ikhale ya ufa wosalala wopanda chotupitsa, wosakaniza ndi mafuta.


Ndipo chopereka chako chikakhala nsembe yaufa ya mumphika, chikhale cha ufa wosalala ndi mafuta.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa