Levitiko 2:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo nsembe yaufa yako ikakhala yokazinga m'chiwaya, ikhale ya ufa wosalala wopanda chotupitsa, wosakaniza ndi mafuta. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo nsembe yaufa yako ikakhala yokazinga m'chiwaya, ikhale ya ufa wosalala wopanda chotupitsa, wosanganiza ndi mafuta. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Nsembe yako ikakhala chakudya chophika pa chitsulo chamoto, chikhale buledi wa ufa wosalala wopanda chofufumitsira, wosakaniza ndi mafuta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ngati nsembe yako yachakudya ndi yophika pa chitsulo chamoto, ikhale ya buledi wa ufa wosalala wopanda yisiti koma wosakaniza ndi mafuta. Onani mutuwo |