Levitiko 15:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo kudetsedwa kwa kukha kwake ndiko: ngakhale chakukhacho chituluka m'thupi mwake, ngakhale chaleka m'thupi mwake, ndiko kumdetsa kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo kudetsedwa kwa kukha kwake ndiko: ngakhale chakukhacho chituluka m'thupi mwake, ngakhale chaleka m'thupi mwake, ndiko kumdetsa kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Lamulo lake lokhudza za kudziipitsa ndi zonyansa zotuluka ku maliseche a munthu nali: malisechewo akamatulutsabe mafinya, kaya aleka, munthuyo ndi woipitsidwa ndithu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Lamulo lokhudza kudziyipitsira ndi zotuluka ku maliseche a munthu nali: Malisechewo akamatulukabe mafinya, kaya aleka, munthuyo adzakhala wodetsedwa: Onani mutuwo |