Levitiko 15:4 - Buku Lopatulika4 Kama aliyense agonapo wakukhayo ali wodetsedwa; ndi chinthu chilichonse achikhalira chili chodetsedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Kama aliyense agonapo wakukhayo ali wodetsedwa; ndi chinthu chilichonse achikhalira chili chodetsedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Bedi lililonse limene munthu wotulutsa mafinyayo agonepo, lidzakhala loipitsidwa. Chinthu chilichonse chimene akhalepo, chidzakhala choipitsidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 “ ‘Bedi lililonse limene munthu wotulutsa mafinyayo agonapo, ndiponso chinthu chilichonse chimene akhalepo chidzakhala chodetsedwa. Onani mutuwo |