Levitiko 15:2 - Buku Lopatulika2 Nenani nao ana a Israele, nimuti nao, Pamene mwamuna aliyense ali ndi nthenda yakukha m'thupi mwake, akhale wodetsedwa, chifukwa cha kukha kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Nenani nao ana a Israele, nimuti nao, Pamene mwamuna aliyense ali ndi nthenda yakukha m'thupi mwake, akhale wodetsedwa, chifukwa cha kukha kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Muuze Aisraele kuti: Mwamuna aliyense akakhala ndi nthenda yotulutsa mafinya ku maliseche ake, zimenezo nzonyansa ndithu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Yankhulani ndi Aisraeli ndipo muwawuze kuti, ‘Mwamuna aliyense akakhala ndi nthenda yotulutsa mafinya ku maliseche ake, zotulukazo ndi zonyansa ndithu. Onani mutuwo |