Levitiko 12:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo akhale m'mwazi wa kumyeretsa kwake masiku makumi atatu kudza atatu; asakhudze kanthu kopatulika, kapena kulowa m'malo opatulika, kufikira adakwanira masiku a kumyeretsa kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo akhale m'mwazi wa kumyeretsa kwake masiku makumi atatu kudza atatu; asakhudze kanthu kopatulika, kapena kulowa m'malo opatulika, kufikira adakwanira masiku a kumyeretsa kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mkaziyo adikirebe masiku ena 33, kuti ayeretsedwe ku matenda ake. Asakhudze kanthu kopatulika kalikonse, ndipo asaloŵe m'malo oyera, mpaka masiku akudziyeretsa atatha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mkaziyo adikire masiku ena 33 kuti ayeretsedwe ku matenda ake. Asakhudze kanthu kalikonse koyera kapena kulowa mʼmalo wopatulika mpaka masiku a kuyeretsedwa kwake atatha. Onani mutuwo |