Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Levitiko 1:8 - Buku Lopatulika

8 ndi ana a Aroni, ansembewo, akonze ziwalozo, mutu, ndi mafuta pa nkhuni zili pa moto wa paguwa la nsembe;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 ndi ana a Aroni, ansembewo, akonze ziwalozo, mutu, ndi mafuta pa nkhuni zili pa moto wa pa guwa la nsembe;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Pamenepo ansembe aike nthuli za nyamayo, mutu wake pamodzi ndi mafuta omwe, pa nkhuni zimene zili pa guwalo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Kenaka ana a Aaroni, wansembe uja, ayike nthuli za nyamayo, mutu wake pamodzi ndi mafuta omwe pa nkhuni zimene zili paguwapo.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 1:8
9 Mawu Ofanana  

Atipatse tsono ng'ombe ziwiri; ndipo adzisankhire iwo eni ng'ombe imodzi, naiduledule, naiike pankhuni osasonkhapo moto; ndipo ine ndidzakonza ng'ombe yinayo, ndi kuiika pankhuni osasonkhapo moto.


Ndipo anakonza nkhunizo, naduladula ng'ombe, naiika pankhuni. Nati, Dzazani madzi mbiya zinai, muwathire pa nsembe yopsereza ndi pankhuni.


Ndi zichiri zangowe, chikhato m'litali mwake, zinamangika m'katimo pozungulirapo; ndi pamagome panali nyama ya nsembe.


Ndipo aikadzule ziwalo zake, pamodzi ndi mutu wake ndi mafuta ake; ndi wansembeyo akonze izi pa nkhuni zili pa moto wa paguwa la nsembe.


Pamenepo abwere nayo nsembe yamoto ya kwa Yehova, yotengako ku nsembe yoyamika; achotse mafuta akukuta matumbo, ndi mafuta onse akukhala pamatumbo,


ndi impso ziwiri, ndi mafuta ali pomwepo okhala m'chuuno, ndi chokuta cha mphafa chofikira kuimpso.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa