Levitiko 1:16 - Buku Lopatulika16 nachotse chitsokomero, ndi chipwidza chake, nazitaye kufupi kwa guwa la nsembe, kum'mawa, kudzala; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 nachotse chitsokomero, ndi chipwidza chake, nazitaye kufupi kwa guwa la nsembe, kum'mawa, kudzala; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono achotse chitsokomero pamodzi ndi nthenga zake zomwe, ndi kuzitaya potayira phulusa, pafupi ndi guwa, cha kuvuma kwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Iye achotse chithokomiro pamodzi ndi nthenga zake zomwe ndi kuzitaya ku malo wotayirako phulusa, kummawa kwa guwalo. Onani mutuwo |