Levitiko 1:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo wansembe abwere nacho ku guwa la nsembe, namwetule mutu wake, naitenthe paguwa la nsembe; ndi mwazi wake aukamulire pa mbali ya guwa la nsembe, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo wansembe abwere nacho ku guwa la nsembe, namwetule mutu wake, naitenthe pa guwa la nsembe; ndi mwazi wake aukamulire pa mbali ya guwa la nsembe, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Wansembe abwere nayo ku guwa, aidule mutu moipotola, ndi kutentha mutuwo paguwapo. Magazi ake aŵathire pansi kuti ayenderere pambali pa guwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Wansembe abwere nayo ku guwa, ayidule mutu moyipotola ndi kutentha mutuwo pa guwa. Magazi ake awathire pansi kuti ayenderere pambali pa guwa. Onani mutuwo |