Levitiko 1:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Yehova anaitana Mose, nanena naye ali m'chihema chokomanako Iye, nati, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Yehova anaitana Mose, nanena naye ali m'chihema chokomanako Iye, nati, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pamene Chauta anali m'chihema chamsonkhano adaitana Mose, namuuza kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 26 Yehova anayitana Mose mu tenti ya msonkhano. Iye anati, Onani mutuwo |