Eksodo 40:38 - Buku Lopatulika38 Pakuti mtambo wa Yehova unakhala pa chihema msana, ndi usiku munali moto m'menemo, pamaso pa mbumba yonse ya Israele, m'maulendo ao onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Pakuti mtambo wa Yehova unakhala pa Kachisi msana, ndi usiku munali moto m'menemo, pamaso pa mbumba yonse ya Israele, m'maulendo ao onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Unkakhala pachihemapo masana, usiku mumtambomo munkayaka moto, ndipo Aisraele onse ankatha kuupenya. Zinkatero pa ulendo wao wonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Kotero mtambo wa Yehova unkakhala pamwamba pa chihema usana, ndi mtambo wamoto umakhala usiku, pamaso pa nyumba yonse ya Israeli pa masiku onse aulendo wawo. Onani mutuwo |