Eksodo 40:37 - Buku Lopatulika37 koma ukapanda kukwera mtambo, samayenda ulendo wao kufikira tsiku loti wakwera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 koma ukapanda kukwera mtambo, samayenda ulendo wao kufikira tsiku loti wakwera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 Koma mtambowo ukapanda kuchoka, Aisraele sankachokanso pachigonopo. Ankadikira tsiku lakuti mtambo wachokapo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Koma ngati mtambo sunachoke, iwo sankasamukanso mpaka tsiku limene udzachoke. Onani mutuwo |