Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 40:36 - Buku Lopatulika

36 Ndipo pakukwera mtambo kuchokera ku chihema, ana a Israele amayenda maulendo ao onse;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 Ndipo pakukwera mtambo kuchokera ku Kachisi, ana a Israele amayenda maulendo ao onse;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Pa maulendo ao onse, mtambo ukachoka pachihemapo, Aisraelewo ankachoka pamene analiripo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 Pa maulendo awo onse, mtambo ukachoka pamwamba pa chihema, Aisraeli ankasamukanso pamene analipo.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 40:36
11 Mawu Ofanana  

koma Inu mwa nsoni zanu zazikulu simunawasiye m'chipululu; mtambo woti njo sunawachokere usana kuwatsogolera m'njira, ngakhale moto wa tolo usiku kuwaunikira panjira anayenera kuyendamo.


Anayala mtambo uwaphimbe; ndi moto uunikire usiku.


Ndipo msana anawatsogolera ndi mtambo ndi usiku wonse ndi kuunika kwa moto.


Ndipo pokwera mtambo kuchokera kuchihema, utatero ana a Israele amayenda ulendo wao; ndipo pamalo pokhala mtambo, pamenepo ana a Israele amamanga mahema ao.


Ngakhale masiku awiri, kapena mwezi, kapena masiku ambiri, pokhalitsa mtambo pamwamba pa chihema ndi kukhalapo, ana a Israele anakhala m'chigono, osayenda ulendo; koma pakukwera uwu, anayenda ulendo.


Pakuti sindifuna, kuti mukhale osadziwa, abale, kuti makolo athu onse anali pansi pa mtambo, naoloka nyanja onse;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa