Hoseya 9:9 - Buku Lopatulika9 Anadzivunditsa kwambiri, monga masiku a Gibea; adzakumbukira mphulupulu yao, adzalanga zochimwa zao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Anadzivunditsa kwambiri, monga masiku a Gibea; adzakumbukira mphulupulu yao, adzalanga zochimwa zao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Anthu aipiratu monga zidachitikira ku Gibea. Nchifukwa chake Mulungu sadzaiŵala kuipa kwao, ndipo adzalanga machimo ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Iwo azama mu zachinyengo monga masiku a Gibeya. Mulungu adzakumbukira zolakwa zawo ndipo adzawalanga chifukwa cha machimo awo. Onani mutuwo |