Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Hoseya 9:5 - Buku Lopatulika

5 Mudzachitanji tsiku la misonkhano yoikika, ndi tsiku la chikondwerero cha Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Mudzachitanji tsiku la masonkhano oikika, ndi tsiku la chikondwerero cha Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Kodi pa tsiku la chikondwerero, tsiku lolemekeza Chauta, anthuwo adzachitapo chiyani?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Kodi mudzachita chiyani pa tsiku la maphwando anu oyikika; pa masiku a zikondwerero za Yehova?

Onani mutuwo Koperani




Hoseya 9:5
4 Mawu Ofanana  

Ndipo mudzachita chiyani tsiku lakudza woyang'anira, ndi chipasuko chochokera kutali? Mudzathawira kwa yani kufuna kuthangatidwa? Mudzasiya kuti ulemerero wanu?


aneneri anenera monyenga nathandiza ansembe pakulamulira kwao; ndipo anthu anga akonda zotere; ndipo mudzachita chiyani pomalizira pake?


Ndidzaleketsanso kusekerera kwake konse, zikondwerero zake, pokhala mwezi pake, ndi masabata ake, ndi misonkhano yake yonse yoikika.


Mudzimangire chiguduli m'chuuno mwanu, nimulire, ansembe inu; bumani otumikira kuguwa la nsembe inu; lowani, gonani usiku wonse m'chiguduli, inu otumikira Mulungu wanga; pakuti nsembe yaufa ndi nsembe yothira zaletsedwera nyumba ya Mulungu wanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa