Hoseya 8:4 - Buku Lopatulika4 Analonga mafumu, koma sikunachokera kwa Ine; anaika akalonga, koma sindinadziwa; anadzipangira mafano a siliva wao ndi golide wao, kuti akalikhidwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Analonga mafumu, koma sikunachokera kwa Ine; anaika akalonga, koma sindinadziwa; anadzipangira mafano a siliva wao ndi golide wao, kuti akalikhidwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 “Amadzilongera mafumu mosatsata kufuna kwanga. Amadziikira atsogoleri popanda chilolezo changa. Adzipangira mafano asiliva ndi agolide, koma adziwononga nawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Amalonga mafumu mosatsata kufuna kwanga. Amasankha akalonga popanda chilolezo changa. Amadzipangira mafano asiliva ndi agolide koma adzawonongeka nawo. Onani mutuwo |