Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Hoseya 8:12 - Buku Lopatulika

12 Ndinamlembera zinthu zambirimbirizo za chilamulo changa, koma zinayesedwa ngati chinthu chachilendo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndinamlembera zinthu zambirimbirizo za chilamulo changa, koma zinayesedwa ngati chinthu chachilendo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Ndidaŵapatsa malamulo ambiri olembedwa, koma saŵasamala. Amaŵayesa achilendo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Ndinawalembera zinthu zambiri za malamulo anga, koma iwo anaziyesa ngati zinthu zachilendo.

Onani mutuwo Koperani




Hoseya 8:12
14 Mawu Ofanana  

Koma anakhala osamvera, napandukira Inu, nataya chilamulo chanu m'mbuyo mwao napha aneneri anu akuwachitira umboni, kuwabwezera kwa Inu, nachita zopeputsa zazikulu.


Munditsegulire maso, kuti ndipenye zodabwitsa za m'chilamulo chanu.


Popeza udana nacho chilangizo, nufulatira mau anga.


Kodi sindinakulembere zoposa za uphungu ndi nzeru;


Pakuti ali anthu opanduka, ana onama, ana osafuna kumva chilamulo cha Yehova;


Ndinawapatsanso malemba anga, ndi kuwadziwitsa maweruzo anga, ndiwo munthu akawachita adzakhala nao ndi moyo.


Anthu anga aonongeka chifukwa cha kusadziwa; popeza unakana kudziwa, Inenso ndikukaniza, kuti usakhale wansembe wanga; popeza waiwala chilamulo cha Mulungu wako, Inenso ndidzaiwala ana ako.


Ndipo potero Myuda aposa ninji? Kapena mdulidwe upindulanji?


Chotero chilamulo chili choyera, ndi chilangizo chake nchoyera, ndi cholungama, ndi chabwino.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa