Hoseya 7:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo sanena m'mtima mwao kuti Ine ndikumbukira zoipa zao zonse; tsopano machitidwe ao awazinga; ali pamaso panga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo sanena m'mtima mwao kuti Ine ndikumbukira zoipa zao zonse; tsopano machitidwe ao awazinga; ali pamaso panga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Koma saganiza kuti Ine sindiiŵala ntchito zao zoipa. Zolakwa zao zaŵazinga, ndipo sizichoka m'maso mwanga.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Koma sazindikira kuti Ine ndimakumbukira zoyipa zawo zonse. Azunguliridwa ndi zolakwa zawo; ndipo sizichoka mʼmaso mwanga. Onani mutuwo |