Hoseya 6:2 - Buku Lopatulika2 Atapita masiku awiri adzatitsitsimutsa, tsiku lachitatu adzatiutsa; ndipo tidzakhala ndi moyo pamaso pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Atapita masiku awiri adzatitsitsimutsa, tsiku lachitatu adzatiutsa; ndipo tidzakhala ndi moyo pamaso pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Posachedwa adzatitsitsimutsa. Patangopita masiku aŵiri kapena atatu, adzatiwukitsa kuti tikhale ndi moyo pamaso pake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Pakapita masiku awiri adzatitsitsimutsa; pa tsiku lachitatu Iye adzatiukitsa kuti tikhale ndi moyo pamaso pake. Onani mutuwo |