Hoseya 5:8 - Buku Lopatulika8 Ombani mphalasa mu Gibea, ndi lipenga mu Rama; fuulani ku Betaveni; pambuyo pako, Benjamini. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ombani mphalasa m'Gibea, ndi lipenga m'Rama; fuulani ku Betaveni; pambuyo pako, Benjamini. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Imbani malipenga ankhondo ku Gibea! Lizani mbetete ku Rama! Chenjezani a ku Betehaveni! Inu a ku Benjamini tsogolani! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 “Womba lipenga mu Gibeya, liza mbetete mu Rama. Fuwulani mfuwu wankhondo mu Beti-Aveni; iwe Benjamini tsogolera. Onani mutuwo |