Hoseya 5:7 - Buku Lopatulika7 Anachita mosakhulupirika pa Yehova, pakuti anabala ana achilendo; mwezi wokhala udzawatha tsopano, pamodzi ndi maiko ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Anachita mosakhulupirika pa Yehova, pakuti anabala ana achilendo; mwezi wokhala udzawatha tsopano, pamodzi ndi maiko ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Adachita zosakhulupirika kwa Chauta, motero ana ao nawonso si ake a Mulungu. Tsono chipembedzo chao chachikunja chidzaŵaonongetsa pamodzi ndi minda yao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iwo ndi osakhulupirika kwa Yehova; amabereka ana amʼchigololo ndipo chikondwerero chawo cha mwezi watsopano chidzawawononga pamodzi ndi minda yawo. Onani mutuwo |