Hoseya 5:6 - Buku Lopatulika6 Adzamuka ndi zoweta zao zazing'ono ndi zazikulu kufunafuna Yehova: koma sadzampeza; Iye wadzibweza kuwachokera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Adzamuka ndi zoweta zao zazing'ono ndi zazikulu kufunafuna Yehova: koma sadzampeza; Iye wadzibweza kuwachokera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Anthu amapereka nsembe zankhosa ndi zang'ombe pofunafuna Chauta, koma samupeza, waŵachokera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Pamene adzapita ndi nkhosa zawo ndi ngʼombe zawo kukapereka nsembe kwa Yehova, iwo sadzamupeza; Iye wawachokera. Onani mutuwo |