Hoseya 5:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo ndikhala kwa Efuremu ngati njenjete, ndi kwa nyumba ya Yuda ngati chivundi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo ndikhala kwa Efuremu ngati njenjete, ndi kwa nyumba ya Yuda ngati chivundi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Nchifukwa chake ndidzaononga Efuremu, monga momwe njenjete zimaonongera nsalu, ndidzakhala ngati chilonda choola pa anthu a ku Yuda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ine ndili ngati njenjete kwa Efereimu, ngati chinthu chowola kwa anthu a ku Yuda. Onani mutuwo |