Hoseya 4:18 - Buku Lopatulika18 Chakumwa chao chasasa, achita uhule kosalekeza; akulu ao akonda manyazi kwambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Chakumwa chao chasasa, achita uhule kosalekeza; akulu ao akonda manyazi kwambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Amati akamwa kwambiri, amangochita zigololo. Amakonda zamanyazi kupambana ulemu wao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ngakhale pamene zakumwa zawo zatha, amapitiriza kuchita zachiwerewere; atsogoleri awo amakonda kwambiri njira zawo zochititsa manyazi. Onani mutuwo |