Hoseya 2:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo kudzakhala tsiku lomwelo, ati Yehova, udzanditcha Mwamuna wanga, osanditchanso Baala wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo kudzakhala tsiku lomwelo, ati Yehova, udzanditcha Mwamuna wanga, osanditchanso Baala wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Nthaŵi imeneyo pondiitana uzidzati, ‘Amuna anga.’ Suzidzatinso, ‘Baala wanga.’ Ndikutero Ine Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 “Tsiku limeneli,” Yehova akuti, “udzandiyitana kuti, ‘Amuna anga;’ sudzandiyitananso kuti, ‘Mbuye wanga.’ Onani mutuwo |