Hoseya 13:7 - Buku Lopatulika7 Chifukwa chake ndikhala nao ngati mkango; ngati nyalugwe ndidzalalira kunjira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Chifukwa chake ndikhala nao ngati mkango; ngati nyalugwe ndidzalalira kunjira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Motero ndidzaŵalumphira ngati mkango, ndidzaŵalalira ngati kambuku m'mbali mwa njira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Motero ndidzawalumphira ngati mkango, ndidzawabisalira mu msewu ngati kambuku. Onani mutuwo |