Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Hoseya 13:12 - Buku Lopatulika

12 Mphulupulu ya Efuremu yamangika, tchimo lake lisungika.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Mphulupulu ya Efuremu yamangika, tchimo lake lisungika.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 “Kuipa kwa anthu a ku Efuremu kwalembedwa m'buku, buku lake la machimo ao ndalisunga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Kulakwa kwa Efereimu kwasungidwa, machimo ake alembedwa mʼbuku.

Onani mutuwo Koperani




Hoseya 13:12
5 Mawu Ofanana  

Cholakwa changa chaikidwa m'thumba lokhomedwa chizindikiro; ndipo mumanga pamodzi mphulupulu zanga.


Mukuti, Mulungu asungira ana ake a munthu choipa chake, ambwezere munthuyo kuti achidziwe.


Pakuti ngakhale usamba ndi soda, ndi kudzitengera sopo wambiri, mphulupulu zako zidziwika pamaso panga, ati Yehova Mulungu.


Koma kolingana ndi kuuma kwako, ndi mtima wako wosalapa, ulikudziunjikira wekha mkwiyo pa tsiku la mkwiyo ndi la kuvumbulutsa kuweruza kolungama kwa Mulungu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa