Hagai 1:3 - Buku Lopatulika3 Pamenepo mau a Yehova anadza mwa Hagai mneneri, ndi kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pamenepo mau a Yehova anadza mwa Hagai mneneri, ndi kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tsono Chauta adapatsa mneneri Hagai uthenga uwu wakuti: Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Tsono Yehova anayankhula ndi mneneri Hagai kuti, Onani mutuwo |