Genesis 9:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo anati, Ayamikike Yehova, Mulungu wa Semu; Kanani akhale kapolo wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo anati, Ayamikike Yehova, Mulungu wa Semu; Kanani akhale kapolo wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 “Atamandike Chauta, Mulungu wa Semu, Kanani adzakhale kapolo wa Semuyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Anatinso, “Atamandike Yehova, Mulungu wa Semu! Kanaani akhale kapolo wa Semu. Onani mutuwo |