Genesis 9:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo anati, Wotembereredwa ndi Kanani; adzakhala kwa abale ake kapolo wa akapolo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo anati, Wotembereredwa ndi Kanani; adzakhala kwa abale ake kapolo wa akapolo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 ndipo adati, “Atembereredwe Kanani! Adzakhala kapolo weniweni wa abale ake.” Popitiriza mau adati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 anati, “Atembereredwe Kanaani! Adzakhala kapolo wa pansi kwenikweni kwa abale ake.” Onani mutuwo |