Genesis 9:24 - Buku Lopatulika24 Nowa ndipo anauka kwa kuledzera kwake, nadziwa chimene anamchitira iye mwana wake wamng'ono. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Nowa ndipo anauka kwa kuledzera kwake, nadziwa chimene anamchitira iye mwana wake wamng'ono. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Nowa atadzuka, adamva zonse zimene mwana wake wamng'onoyo adaachita, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Nowa atadzuka, kuledzera kutatha, ndikudziwa zimene mwana wake wamngʼono wamwamuna uja anamuchitira, Onani mutuwo |