Genesis 9:21 - Buku Lopatulika21 namwa vinyo wake, naledzera; ndipo anali wamaliseche m'kati mwa hema wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 namwa vinyo wake, naledzera; ndipo anali wamaliseche m'kati mwa hema wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Tsiku lina atangomwa vinyo, adaledzera, ndipo adavula zovala zake zonse, nakagona ali maliseche m'hema mwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Tsiku lina pamene Nowa anamwako vinyo wa zipatso za mʼmundawo analedzera ndipo anavula zovala zake zonse ndi kugona mu tenti yake ali maliseche. Onani mutuwo |