Genesis 9:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Mulungu anadalitsa Nowa ndi ana ake, nati kwa iwo, Mubalane, muchuluke, mudzaze dziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Mulungu anadalitsa Nowa ndi ana ake, nati kwa iwo, Mubalane, muchuluke, mudzaze dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Mulungu adadalitsa Nowa ndi ana ake omwe, nati “Mubale ana ambiri ndi kuchulukana, kuti mudzaze dziko lonse lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ndipo Mulungu anadalitsa Nowa ndi ana ake aamuna nati kwa iwo, “Berekanani ndipo muchulukane ndi kudzaza dziko lapansi. Onani mutuwo |