Genesis 8:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo analindanso masiku ena asanu ndi awiri; natulutsa njiwayo: ndipo siinabwerenso konse kwa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo analindanso masiku ena asanu ndi awiri; natulutsa njiwayo: ndipo siinabweranso konse kwa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pambuyo pake Nowa atadikiranso masiku ena asanu ndi aŵiri, adaitulutsanso nkhunda ija, koma nkhundayo sidabwererenso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Iye anadikira masiku ena asanu ndi awiri ndipo anatumizanso nkhunda ija, koma nthawi imeneyi sinabwererenso kwa iye. Onani mutuwo |