Genesis 7:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo analowa Nowa ndi ana ake ndi mkazi wake ndi akazi a ana ake m'chingalawamo, chifukwa cha madzi a chigumula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo analowa Nowa ndi ana ake ndi mkazi wake ndi akazi a ana ake m'chingalawamo, chifukwa cha madzi a chigumula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Iyeyo ndi mkazi wake ndi ana ake aamuna ndi akazi ao adaloŵa m'chombo, kuthaŵa chigumulacho. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ndipo Nowa, ana ake aamuna, mkazi wake, pamodzi ndi ana ake aakazi analowa mu chombo chija kuthawa madzi a chigumula. Onani mutuwo |