Genesis 7:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo madzi anapambana ndithu padziko lapansi; anamizidwa mapiri aatali onse amene anali pansi pathambo lonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo madzi anapambana ndithu pa dziko lapansi; anamizidwa mapiri aatali onse amene anali pansi pa thambo lonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Kukwera kwa madzi kudapitirira ndithu mpaka kumiza ndi mapiri aatali omwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Madzi a chigumula anabwerabe molimbika motero kuti mapiri ataliatali onse a pa dziko anamizidwa. Onani mutuwo |