Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 7:18 - Buku Lopatulika

18 Ndipo madzi anapambana, nachuluka ndithu padziko lapansi, ndipo chingalawa chinayandama pamadzi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Ndipo madzi anapambana, nachuluka ndithu pa dziko lapansi, ndipo chingalawa chinayandama pamadzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Madziwo adanka nakwererakwerera, ndipo chombocho chidayandama pa madzi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Madzi anafika mwamphamvu ndipo anachulukirachulukira pa dziko lapansi moti chombo chinayandama pamwamba pa madziwo.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 7:18
6 Mawu Ofanana  

Ndipo chigumula chinali padziko lapansi masiku makumi anai: ndipo madzi anachuluka natukula chingalawa, ndipo chinakwera pamwamba padziko lapansi.


Ndipo madzi anapambana ndithu padziko lapansi; anamizidwa mapiri aatali onse amene anali pansi pathambo lonse.


Amene anakwatulidwa isanafike nyengo yao, chigumula chinakokolola kuzika kwao;


M'mwemo muyenda zombo; ndi Leviyatani amene munamlenga aseweremo.


Chigumula chisandifotsere, ndipo chakuya chisandimize; ndipo asanditsekere pakamwa pake pa dzenje.


Popeza madziwo anabwerera, namiza magaleta ndi apakavalo, ndiwo nkhondo yonse ya Farao imene idalowa pambuyo pao m'nyanja; sanatsale wa iwowa ndi mmodzi yense.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa