Genesis 7:16 - Buku Lopatulika16 Zimene zinalowazo, zinalowa yamphongo ndi yaikazi zamoyo zonse, monga momwe Mulungu anamlamulira iye: ndipo Yehova anamtsekera iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Zimene zinalowazo, zinalowa yamphongo ndi yaikazi zamoyo zonse, monga momwe Mulungu anamlamulira iye: ndipo Yehova anamtsekera iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 monga Mulungu adaalamulira. Pomwepo Chauta adatseka pa khomo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Iye analowa nazo zazimuna ndi zazikazi monga mmene Mulungu anamulamulira. Kenaka Yehova anatseka pa khomo. Onani mutuwo |