Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 7:15 - Buku Lopatulika

15 Ndipo zinalowa kwa Nowa m'chingalawamo ziwiriziwiri zamoyo zonse, m'mene muli mpweya wa moyo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ndipo zinalowa kwa Nowa m'chingalawamo ziwiriziwiri zamoyo zonse, m'mene muli mpweya wa moyo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Nowa adaloŵa m'chombomo pamodzi ndi zamoyo zonse zazimuna ndi zazikazi,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Nowa analowa mu chombo muja pamodzi ndi zamoyo zonse.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 7:15
5 Mawu Ofanana  

iwo, ndi zamoyo zonse monga mwa mitundu yao, ndi zinyama zonse monga mwa mitundu yao, zokwawa zonse zokwawa padziko lapansi monga mwa mitundu yao, ndi zouluka zonse monga mwa mitundu yao, ndi mbalame zonse za mitundumitundu.


Zimene zinalowazo, zinalowa yamphongo ndi yaikazi zamoyo zonse, monga momwe Mulungu anamlamulira iye: ndipo Yehova anamtsekera iye.


zinalowa ziwiriziwiri kwa Nowa m'chingalawamo, yamphongo ndi yaikazi, monga momwe Mulungu anamlamulira Nowa.


Mmbulu udzakhala pamodzi ndi mwanawankhosa, ndipo nyalugwe adzagona pansi ndi mwanawambuzi; ndipo mwanawang'ombe ndi mwana wa mkango ndi choweta chonenepa pamodzi; ndipo mwana wamng'ono adzazitsogolera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa